Levitiko 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+ Salimo 73:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti onse okhala kutali ndi inu adzatheratu.+Mudzawononga ndithu aliyense wochita chigololo mwa kukusiyani.+ Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+
27 Pakuti onse okhala kutali ndi inu adzatheratu.+Mudzawononga ndithu aliyense wochita chigololo mwa kukusiyani.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+