2 Mafumu 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanga maguwa ansembe m’nyumba ya Yehova,+ imene ponena za iyo Yehova anati: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+ 2 Mbiri 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanga maguwa ansembe+ m’nyumba ya Yehova, imene ponena za iyo Yehova anati: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+ Yeremiya 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa+ ndipo m’nyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ watero Yehova. Yeremiya 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo anaika zinthu zawo zonyansa m’nyumba imene imatchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+
4 Anamanga maguwa ansembe m’nyumba ya Yehova,+ imene ponena za iyo Yehova anati: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+
4 Anamanga maguwa ansembe+ m’nyumba ya Yehova, imene ponena za iyo Yehova anati: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+
11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa+ ndipo m’nyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ watero Yehova.