Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Mfumu Ahazi+ inapita kukakumana ndi Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ku Damasiko. Kumeneko inaonako guwa lansembe,+ chotero Mfumu Ahazi inatumizira wansembe Uliya chitsanzo cha kamangidwe ka guwa lansembe lonselo.+

  • 2 Mbiri 34:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kuwonjezera apo, anthu anagwetsa maguwa ansembe+ a Abaala+ pamaso pake, ndipo zofukizira+ zimene zinali pamwamba pa maguwawo iye anazigumula. Mizati yopatulika,+ zifaniziro zogoba,+ ndi zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula, anaziphwanya n’kuziperapera.+ Phulusa lakelo analiwaza pamanda a anthu amene anali kupereka nsembe kwa zinthu zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena