Ekisodo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anatenga mwana wa ng’ombe amene iwo anapanga n’kumutentha ndi moto ndi kum’pera mpaka atakhala fumbi.+ Kenako anamwaza fumbilo pamadzi+ ndi kuwamwetsa Aisiraeli.+ Deuteronomo 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+
20 Ndiyeno anatenga mwana wa ng’ombe amene iwo anapanga n’kumutentha ndi moto ndi kum’pera mpaka atakhala fumbi.+ Kenako anamwaza fumbilo pamadzi+ ndi kuwamwetsa Aisiraeli.+
21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+