Numeri 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Aisiraeli anayamba kupembedza nawo Baala wa ku Peori.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unawayakira.+ Oweruza 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anasiya Yehova ndi kuyamba kutumikira Baala ndi zifaniziro za Asitoreti.+ 2 Mbiri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+ Yeremiya 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wa makamu, Wokubzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a m’nyumba ya Isiraeli+ ndi a m’nyumba ya Yuda achita ndi kundikhumudwitsa nazo pofukizira Baala nsembe zautsi.”+
3 Chotero Aisiraeli anayamba kupembedza nawo Baala wa ku Peori.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unawayakira.+
2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+
17 “Yehova wa makamu, Wokubzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a m’nyumba ya Isiraeli+ ndi a m’nyumba ya Yuda achita ndi kundikhumudwitsa nazo pofukizira Baala nsembe zautsi.”+