Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+

  • Yoswa 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kodi cholakwa chimene tinachita ku Peori+ chatichepera? Kufikira lero, sitinadziyeretsebe ku cholakwa chimene chija, ngakhale kuti mliri unagwera khamu la Yehova.+

  • Salimo 106:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anayamba kulambira Baala wa ku Peori,+

      Ndi kudya nsembe zoperekedwa ku zinthu zakufa.+

  • Hoseya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Isiraeli ndinamupeza ali ngati mphesa zam’chipululu.+ Ndinaona makolo a anthu inu ali ngati nkhuyu zoyambirira pamtengo wa mkuyu wongoyamba kumene kubereka.+ Iwo anapita kwa Baala wa ku Peori+ ndipo anadzipereka kwa chinthu chochititsa manyazicho.+ Anakhala onyansa ngati chinthu chimene anali kuchikondacho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena