Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu.

  • Yesaya 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Nkhata yamaluwa yokongola imene maluwa ake akufota,+ yomwe ili pamwamba pa phiri m’chigwa chachonde, idzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha+ chilimwe chisanafike, imene munthu akaiona amaithyola n’kuimeza msangamsanga.

  • Mika 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsoka kwa ine,+ chifukwa ndakhala ngati munthu wanjala amene sanapeze zipatso kuti adye.+ Ndakhala ngati munthu amene sanapeze nkhuyu zoyambirira zimene anali kuzilakalaka, nthawi yokolola zipatso za m’chilimwe* ndi mphesa itatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena