Yakobo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+
10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+