Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 17:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’dzikolo mudzangotsala zokunkha ngati mmene zimatsalira mumtengo wa maolivi akaugwedeza: pamwamba pa nthambi padzangokhala maolivi awiri kapena atatu akupsa. Panthambi zobala zipatso padzangokhala maolivi anayi kapena asanu okha,” akutero Yehova, Mulungu wa Isiraeli.+

  • Yesaya 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+

  • Yeremiya 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova wa makamu wanena kuti: “Mosalephera adani adzakunkha otsalira a Isiraeli ngati mmene amakunkhira mphesa.+ Kweza dzanja lako ngati munthu amene akuthyola mphesa panthambi za mtengo wa mpesa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena