Yesaya 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼdzikomo mudzangotsala zokunkha zokhaNgati mmene zimatsalira mumtengo wa maolivi akaugwedeza: Panthambi imene ili pamwamba kwambiri pamangotsala maolivi awiri kapena atatu okha akupsa.Panthambi zake zobala zipatso pamangotsala maolivi 4 kapena 5 okha,”+ akutero Yehova, Mulungu wa Isiraeli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:6 Yesaya 1, tsa. 196
6 Mʼdzikomo mudzangotsala zokunkha zokhaNgati mmene zimatsalira mumtengo wa maolivi akaugwedeza: Panthambi imene ili pamwamba kwambiri pamangotsala maolivi awiri kapena atatu okha akupsa.Panthambi zake zobala zipatso pamangotsala maolivi 4 kapena 5 okha,”+ akutero Yehova, Mulungu wa Isiraeli.