Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko.

  • Deuteronomo 24:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Pokolola maolivi mwa kukwapula mitengo yake, usabwerere m’mbuyo kukaona ngati m’nthambi zake muli zipatso zotsala. Zimenezo zikhale za mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+

  • Oweruza 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero iye anawayankha kuti: “Kodi ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?+ Kodi zokunkha za Efuraimu+ si zabwino kwambiri kuposa mphesa zimene Abi-ezeri+ wakolola?

  • Yesaya 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+

  • Aroma 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena