Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Nkhuyu zimene zinali m’dengu limodzi zinali zabwino kwambiri ngati nkhuyu zoyamba kucha.+ Koma nkhuyu zimene zinali m’dengu lina zinali zoipa kwambiri moti munthu sakanatha kuzidya chifukwa cha kuipa kwake.

  • Nahumu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Malo ako onse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri ali ngati mitengo ya mkuyu imene ili ndi nkhuyu zoyambirira kupsa. Munthu akagwedeza mitengoyo, nkhuyu zakezo zimagwera m’kamwa mwa munthu wozidya.+

  • Chivumbulutso 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nyenyezi zakumwamba zinagwera kudziko lapansi, ngati mmene mkuyu wogwedezeka ndi mphepo yamphamvu umagwetsera nkhuyu zake zosapsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena