Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 66:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Munthu amene akupha ng’ombe yamphongo ali ngati wopha munthu.+ Amene akupereka nsembe ya nkhosa ali ngati wothyola khosi la galu.+ Wopereka mphatso ali ngati wopereka magazi a nkhumba.+ Wopereka lubani wachikumbutso+ ali ngati wopereka dalitso pogwiritsa ntchito mawu onenerera zamatsenga.+ Anthuwo asankha njira zawozawo, ndipo amasangalala ndi zinthu zawo zonyansa.+

  • Ezekieli 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense akunyada chifukwa cha chinthu chake chokongoletsera. Iwo agwiritsira ntchito siliva ndi golide kupangira mafano awo onyansa,+ ndi zinthu zawo zonyansa.+ N’chifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzaipidwe nazo.+

  • Amosi 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Perekani nsembe zoyamikira zautsi kuchokera pa zinthu zokhala ndi chofufumitsa+ ndipo lengezani ndi kufalitsa za nsembe zaufulu+ pakuti ndi zimene mukukonda, inu ana a Isiraeli,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena