1 Samueli 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+ Yesaya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musabweretsenso nsembe zina zaufa zopanda phindu.+ Zofukiza zanu ndikunyansidwa nazo.+ Mumasunga masiku okhala mwezi+ ndi sabata,+ ndipo mumaitanitsa misonkhano.+ Koma ine ndatopa kukuonani mukugwiritsira ntchito mphamvu zamatsenga+ pamene mukuchita misonkhano yapadera.
23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+
13 Musabweretsenso nsembe zina zaufa zopanda phindu.+ Zofukiza zanu ndikunyansidwa nazo.+ Mumasunga masiku okhala mwezi+ ndi sabata,+ ndipo mumaitanitsa misonkhano.+ Koma ine ndatopa kukuonani mukugwiritsira ntchito mphamvu zamatsenga+ pamene mukuchita misonkhano yapadera.