Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Malaki 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova adzapha ndi kuchotsa munthu aliyense wochita zonyansazi+ m’mahema a Yakobo. Iye adzapha ndi kuchotsamo aliyense, kaya akhale ndani.* Komanso adzapha aliyense amene akupereka nsembe ngati mphatso+ kwa Yehova wa makamu.”

  • Luka 11:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Tsoka inu Afarisi, chifukwa mumapereka chakhumi+ cha timbewu ta minti ndi ta luwe, ndi cha mbewu zakudimba zamtundu uliwonse. Koma mumanyalanyaza chilungamo ndi chikondi cha Mulungu! Unalidi udindo wanu kuchita zinthu zimenezi, koma simunayenera kusiya zinazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena