1 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo. Amosi 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+
22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.
22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+