Yeremiya 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Pakuti ana a Yuda achita zinthu zoipa m’maso mwanga,’ watero Yehova. ‘Aika zinthu zawo zonyansa m’nyumba yotchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+ Yeremiya 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo anaika zinthu zawo zonyansa m’nyumba imene imatchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+
30 ‘Pakuti ana a Yuda achita zinthu zoipa m’maso mwanga,’ watero Yehova. ‘Aika zinthu zawo zonyansa m’nyumba yotchedwa ndi dzina langa kuti aiipitse.+