Ekisodo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+ Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+ Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+
13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+
7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+
2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+