Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+ Zekariya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine Yehova ndidzawachititsa kukhala amphamvu+ ndipo zochita zawo zidzalemekeza dzina langa,’+ watero Yehova.”
31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+
12 Ine Yehova ndidzawachititsa kukhala amphamvu+ ndipo zochita zawo zidzalemekeza dzina langa,’+ watero Yehova.”