Salimo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+ Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+
9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+