Deuteronomo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Monga mmene chiwombankhanga chimagwedezera mwamphamvu chisa chake,Mmene chimaulukira pamwamba pa ana ake,+Mmene chimatambasulira mapiko ake, ndi kutenga anawo,N’kuwanyamula pamapiko ake,+ Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+ Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+
11 Monga mmene chiwombankhanga chimagwedezera mwamphamvu chisa chake,Mmene chimaulukira pamwamba pa ana ake,+Mmene chimatambasulira mapiko ake, ndi kutenga anawo,N’kuwanyamula pamapiko ake,+ Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+ Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+
71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+
11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+