Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+ Mika 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtundu uliwonse wa anthu udzayenda m’dzina la mulungu wake.+ Koma ife tidzayenda m’dzina la Yehova Mulungu wathu+ mpaka kalekale, inde mpaka muyaya.+
5 Mtundu uliwonse wa anthu udzayenda m’dzina la mulungu wake.+ Koma ife tidzayenda m’dzina la Yehova Mulungu wathu+ mpaka kalekale, inde mpaka muyaya.+