2 Mafumu 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mtundu uliwonse unapanga mulungu wake+ n’kukamuika m’kachisi m’malo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi m’mizinda imene unali kukhala. Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+
29 Koma mtundu uliwonse unapanga mulungu wake+ n’kukamuika m’kachisi m’malo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi m’mizinda imene unali kukhala.
11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+