Numeri 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova akuyang’aneni mokondwera+ ndipo akupatseni mtendere.”’+ Salimo 72:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+ Salimo 147:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akukhazikitsa mtendere m’dziko lako.+Ndipo akupitirizabe kukukhutiritsa ndi tirigu wabwino koposa.+ Aroma 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mulungu amene amapatsa mtendere akhale ndi nonsenu.+ Ame. 1 Akorinto 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukoma mtima kwakukulu+ ndi mtendere+ zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu+ zikhale ndi inu.
7 M’masiku ake, wolungama adzaphuka,+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka kwa nthawi yonse pamene mwezi udzakhalepo.+
14 Iye akukhazikitsa mtendere m’dziko lako.+Ndipo akupitirizabe kukukhutiritsa ndi tirigu wabwino koposa.+
3 Kukoma mtima kwakukulu+ ndi mtendere+ zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu+ zikhale ndi inu.