Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+

  • Salimo 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+

      Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+

  • Salimo 122:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu, anthu inu.+

      Amene amakukonda, mzinda iwe, sadzakhala ndi nkhawa iliyonse.+

  • Yesaya 45:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+ Ndimabweretsa mtendere+ ndiponso tsoka.+ Ine Yehova ndimapanga zonsezi.+

  • Yesaya 60:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 M’malo mwa mkuwa, ndidzabweretsa golide.+ M’malo mwa chitsulo, ndidzabweretsa siliva. M’malo mwa mtengo, ndidzabweretsa mkuwa ndipo m’malo mwa miyala, ndidzabweretsa chitsulo. Ndidzaika mtendere kuti ukhale ngati wokuyang’anira,+ ndi chilungamo kuti chikhale ngati wokupatsa ntchito.+

  • Aroma 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mulungu amene amapatsa mtendere akhale ndi nonsenu.+ Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena