1 Mbiri 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli. Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+ Hagai 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.” Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.
9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli.
9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.”
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.