Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ziwiya zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndipo ziwiya zonse za m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali za golide woyenga bwino.+ Panalibe chiwiya chasiliva. Siliva sankaoneka ngati kanthu m’masiku a Solomo.

  • Chivumbulutso 21:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mpandawo unali womangidwa ndi mwala wa yasipi,+ ndipo mzindawo unali womangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena