2 Mbiri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ziwiya zonse zomweramo+ Mfumu Solomo zinali zagolide,+ ndipo ziwiya zonse za m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali zagolide woyenga bwino. Panalibe chiwiya chasiliva. Siliva sankaoneka ngati kanthu+ m’masiku a Solomo,
20 Ziwiya zonse zomweramo+ Mfumu Solomo zinali zagolide,+ ndipo ziwiya zonse za m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali zagolide woyenga bwino. Panalibe chiwiya chasiliva. Siliva sankaoneka ngati kanthu+ m’masiku a Solomo,