Esitere 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anali kulandira vinyo m’ziwiya zagolide.+ Chiwiya chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake, ndipo vinyo amene mfumu inapereka+ anali wochuluka kwambiri, moti ndi mfumu yokha imene ikanatha kupereka vinyo wochuluka choncho.
7 Anthu anali kulandira vinyo m’ziwiya zagolide.+ Chiwiya chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake, ndipo vinyo amene mfumu inapereka+ anali wochuluka kwambiri, moti ndi mfumu yokha imene ikanatha kupereka vinyo wochuluka choncho.