1 Mafumu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ziwiya zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndipo ziwiya zonse za m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali za golide woyenga bwino.+ Panalibe chiwiya chasiliva. Siliva sankaoneka ngati kanthu m’masiku a Solomo.
21 Ziwiya zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndipo ziwiya zonse za m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali za golide woyenga bwino.+ Panalibe chiwiya chasiliva. Siliva sankaoneka ngati kanthu m’masiku a Solomo.