Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Mulungu anati:+ “Pakhale kuwala.” Ndipo kuwala kunakhalapo.+

  • Salimo 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+

      Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+

  • Yeremiya 31:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Yehova ndiye Wopereka dzuwa kuti liziwala masana,+ woikira mwezi malamulo,+ wopereka nyenyezi+ kuti ziziwala usiku,+ amene amavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Wochita zimenezi dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye wanena kuti:

  • Yakobo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena