Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 104:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Wapanga mwezi kuti uzisonyeza nthawi yoikidwiratu.+

      Dzuwa nalo limadziwa bwino kumene limalowera.+

  • Yesaya 40:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Kwezani maso anu kumwamba muone. Kodi ndani amene analenga zinthu zimenezo?+ Ndi amene akutsogolera gulu lonse la nyenyezizo malinga ndi chiwerengero chake, ndipo amaziitana potchula iliyonse dzina lake.+ Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake zoopsa,+ ndiponso chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zambiri zochitira zinthu, palibe imene imasowa.

  • Mateyu 5:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake pa anthu oipa ndi abwino, ndi kuvumbitsira mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena