Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Motero Mulungu anapanga zounikira zikuluzikulu ziwiri. Chounikira chokulirapo anachipanga kuti chilamulire usana, ndi chocheperapo kuti chilamulire usiku, komanso nyenyezi.+

  • Salimo 136:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Amene anapanga mwezi ndi nyenyezi kuti zizilamulira pamodzi usiku:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 31:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Yehova ndiye Wopereka dzuwa kuti liziwala masana,+ woikira mwezi malamulo,+ wopereka nyenyezi+ kuti ziziwala usiku,+ amene amavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Wochita zimenezi dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye wanena kuti:

  • 1 Akorinto 15:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ulemerero wa dzuwa+ ndi wosiyana ndi ulemerero wa mwezi,+ ndipo ulemerero wa nyenyezi ndi winanso. Ngakhale ulemerero wa nyenyezi+ ina, umasiyana ndi ulemerero wa inzake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena