Danieli 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.
3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.