Genesis 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndi kuti zilamulire usana ndi usiku, komanso zilekanitse kuwala ndi mdima.+ Zitatero, Mulungu anaona kuti zili bwino.+ Yobu 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati ndinkaona kuwala kukamanyezimira,Kapena mwezi wamtengo wapatali ukuyenda,+ Salimo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
18 ndi kuti zilamulire usana ndi usiku, komanso zilekanitse kuwala ndi mdima.+ Zitatero, Mulungu anaona kuti zili bwino.+
26 Ngati ndinkaona kuwala kukamanyezimira,Kapena mwezi wamtengo wapatali ukuyenda,+ Salimo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+