Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.+ Yesaya 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+ 2 Akorinto 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere, zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+
12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+
2 Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere, zochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+