Aroma 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikulembera inu nonse amene muli ku Roma monga okondedwa a Mulungu, oitanidwa+ kukhala oyera:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ wochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye wathu Yesu Khristu+ zikhale ndi inu. Aefeso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu. Afilipi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kukoma mtima kwakukulu, ndi mtendere wochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi kwa Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+
7 Ndikulembera inu nonse amene muli ku Roma monga okondedwa a Mulungu, oitanidwa+ kukhala oyera:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ wochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye wathu Yesu Khristu+ zikhale ndi inu.
3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.
2 Kukoma mtima kwakukulu, ndi mtendere wochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi kwa Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+