Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pa tsiku labwino ukhale munthu wabwino,+ ndipo pa tsiku latsoka uzindikire kuti Mulungu woona anapanga masiku onsewa mofanana,+ ndi cholinga chakuti anthu asadziwe chilichonse chimene chidzachitike pambuyo pawo.+

  • Yesaya 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+

  • Yeremiya 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+

  • Amosi 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena