Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Zefaniya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku limenelo, lipenga la nyanga ya nkhosa ndiponso chizindikiro chochenjeza zidzalira+ pochenjeza mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, komanso nsanja zazitali kwambiri za m’makona.+
5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
16 Pa tsiku limenelo, lipenga la nyanga ya nkhosa ndiponso chizindikiro chochenjeza zidzalira+ pochenjeza mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, komanso nsanja zazitali kwambiri za m’makona.+