Genesis 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+ Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+
35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli ukakhale kumeneko.+ Ukamangire guwa lansembe Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unali kuthawa Esau m’bale wako.”+
4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+