Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+ 1 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+
4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+