Yoswa 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Adoni-zedeki anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibeoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndiponso amuna onse a kumeneko anali amphamvu. Yoswa 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti,
2 Adoni-zedeki anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibeoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndiponso amuna onse a kumeneko anali amphamvu.