Maliro 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.
8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.