Yobu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ikani dzanja lanu kutali ndi ine,Ndipo kuopsa kwanu kusandichititse mantha.+ Maliro 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+
2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+