Yesaya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzagwetsa mzinda wokhala ndi mipanda yachitetezo italiitali yolimba kwambiri. Adzautsitsa n’kuugwetsera pansi, pafumbi.+ Yesaya 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+
12 Iye adzagwetsa mzinda wokhala ndi mipanda yachitetezo italiitali yolimba kwambiri. Adzautsitsa n’kuugwetsera pansi, pafumbi.+
5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+