Deuteronomo 28:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Chotero adzakuzungulirani m’mizinda yanu yonse kufikira mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene muzidzaidalira itagwa m’dziko lanu lonse. Adzakuzungulirani ndithu m’mizinda yanu yonse m’dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ Mika 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzagwetsa mizinda ya m’dziko lanu. Ndidzagumula malo anu onse amene ali ndi mipanda yolimba kwambiri.+
52 Chotero adzakuzungulirani m’mizinda yanu yonse kufikira mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene muzidzaidalira itagwa m’dziko lanu lonse. Adzakuzungulirani ndithu m’mizinda yanu yonse m’dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
11 Ine ndidzagwetsa mizinda ya m’dziko lanu. Ndidzagumula malo anu onse amene ali ndi mipanda yolimba kwambiri.+