Yesaya 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna za panyumba+ ya mfumu ya ku Babulo.’”+ Yesaya 43:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero ndidzadetsa akalonga a pamalo oyera. Yakobo ndidzamuwononga ndipo Isiraeli ndidzamunyozetsa.+
7 ‘Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna za panyumba+ ya mfumu ya ku Babulo.’”+
28 Chotero ndidzadetsa akalonga a pamalo oyera. Yakobo ndidzamuwononga ndipo Isiraeli ndidzamunyozetsa.+