Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+
29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+