Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pamene anamwali+ anasonkhanitsidwa pamodzi kachiwiri, Moredekai anali atakhala pansi kuchipata cha mfumu.+

  • Esitere 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho atumiki onse a mfumu amene anali kuchipata cha mfumu+ anali kuwerama ndi kugwadira Hamani, pakuti mfumu inali italamula kuti anthu azim’chitira zimenezi. Koma Moredekai sanali kumuweramira kapena kumugwadira.+

  • Yeremiya 39:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno akalonga onse a mfumu ya Babulo analowa mumzindamo ndi kukhala pansi ku Chipata cha Pakati.+ Mayina a akalongawo anali Nerigali-sarezera, Samugari-nebo, Sarisekimu, Rabisarisi,* Nerigali-sarezera amene anali Rabimagi* ndi akalonga ena onse a mfumu ya Babulo.

  • Amosi 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena