Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Patapita nthawi, Yehoyakini mfumu ya Yuda anatuluka n’kupita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake,+ atumiki ake, akalonga ake, ndi nduna za panyumba yake, ndipo mfumu ya Babuloyo inam’tengera Yehoyakini ku ukapolo m’chaka cha 8+ cha ufumu wake.

  • 2 Mafumu 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Akasidiwo anagwira mfumuyo+ n’kupita nayo ku Ribila+ kwa mfumu ya Babulo, kuti akaiuze chigamulo chake.

  • 2 Mbiri 33:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pomalizira pake Yehova anawabweretsera+ akuluakulu a asilikali a mfumu ya Asuri.+ Iwo anagwira Manase akubisala m’dzenje.+ Atatero anam’manga+ ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.

  • Ezekieli 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Chonde, uza nyumba yopandukayi+ kuti, ‘Kodi anthu inu simukudziwa tanthauzo la zinthu zimenezi?’ Auze kuti, ‘Mfumu ya Babulo inabwera ku Yerusalemu n’kudzatenga mfumu+ ndi akalonga a mumzindawo ndi kupita nawo ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena